13 Pakuti ndikadagona pansi pomwepo ndi kukhala cete;Ndikanagona tulo; pamenepo ndikadaona popumula;
Werengani mutu wathunthu Yobu 3
Onani Yobu 3:13 nkhani