1 Koma tsopano iwo osafikana msinkhu wanga andiseka,Iwo amene atate ao ndikadawapeputsa, osawaika pamodzi ndi agaru olinda nkhosa zanga.
Werengani mutu wathunthu Yobu 30
Onani Yobu 30:1 nkhani