Yobu 32:1 BL92

1 Pamenepo amuna atatuwa analeka kumyankha Yobu; pakuti anali wolungama pamaso pace pa iye mwini.

Werengani mutu wathunthu Yobu 32

Onani Yobu 32:1 nkhani