26 Taonani, Mulungu ndiye wamkuru, ndipo sitimdziwa;Ciwerengo ca zaka zace ncosasanthulika.
Werengani mutu wathunthu Yobu 36
Onani Yobu 36:26 nkhani