16 Ndipo zitatha izi, Yobu anakhala ndi moyo zaka zana limodzi mphambu makumi anai, naona ana ace ndi zidzukulu zace mibadwo inai.
Werengani mutu wathunthu Yobu 42
Onani Yobu 42:16 nkhani