Yobu 42:7 BL92

7 Kunali tsono atanena Yehova mau awa kwa Yobu, Yehova anati kwa Elifazi wa ku Temani, Mkwiyo wanga wakuyakira iwe ndi mabwenzi ako awiri, pakuti simunandinenera coyenera monga ananena mtumiki wanga Yobu.

Werengani mutu wathunthu Yobu 42

Onani Yobu 42:7 nkhani