Yobu 6:4 BL92

4 Pakuti mibvi ya Wamphamvuyonse yandilowa,Mzimu wanga uumwa ulembe wace;Zoopsa za Mulungu zindindandira nkhondo.

Werengani mutu wathunthu Yobu 6

Onani Yobu 6:4 nkhani