Macitidwe 10:12 BL92

12 m'menemo munali nyama za miyendo inai za mitundu yonse, ndi zokwawa za padziko ndi mbalame za m'mlengalenga.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 10

Onani Macitidwe 10:12 nkhani