17 Ndipo pokayika-kayika Petro mwa yekha ndi kuti masomphenya adawaona akuti ciani, taonani, amuna aja otumidwa ndi Komeliyo, atafunsira nyumba ya Simoni, anaima pa cipata,
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 10
Onani Macitidwe 10:17 nkhani