23 Pamenepo anawalowetsa nawacereza.Ndipo m'mawa mwace ananyamuka naturuka nao, ndi ena a abale a ku Yopaanamperekezaiye.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 10
Onani Macitidwe 10:23 nkhani