Macitidwe 11:13 BL92

13 ndipo anatiuza ife kuti adaona mngelo wakuimirira m'nyumba yace, ndi kuti, Tumiza anthu ku Yopa, akaitane Simoni, wonenedwanso Petro;

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 11

Onani Macitidwe 11:13 nkhani