Macitidwe 12:4 BL92

4 Ndipo m'mene adamgwira, anamuika m'ndende, nampereka kwa magulu anai a alonda, lonse anai anai, amdikire iye; ndipo anafuna kumturutsa kudza naye kwa anthu atapita Paskha.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 12

Onani Macitidwe 12:4 nkhani