Macitidwe 12:7 BL92

7 Ndipo taonani, mngelo wa Ambuye anaimirirapo, ndipo kuunika kunawala mokhalamo iye; ndipo anakhoma Petro m'nthiti, namuutsa iye, nanena, Tauka msanga, Ndipo maunyolo anagwa kucoka m'manja mwace.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 12

Onani Macitidwe 12:7 nkhani