Macitidwe 13:17 BL92

17 Mulungu wa anthu awa Israyeli anasankha makolo athu, nakweza anthuwo pakugonerera iwo m'dziko la Aigupto, ndipo ndi dzanja lokwezeka anawaturutsa iwo m'menemo.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 13

Onani Macitidwe 13:17 nkhani