Macitidwe 13:22 BL92

22 Ndipo m'mene atamcotsa iye, anawautsira Davine akhale mfumu yao; amenenso anamcitira umboni, nati, Ndapeza Davine, mwana wa Jese, munthu wa pamtima panga, amene adzacita cifuniro canga conse.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 13

Onani Macitidwe 13:22 nkhani