25 Ndipo pakukwaniritsa njira yace Yohane, ananena, Muyesa kuti ine ndine yani? Ine sindine iye. Koma taonani, akudza wina wonditsata ine, amene sindiyenera kummasulira nsapato za pa mapazi ace.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 13
Onani Macitidwe 13:25 nkhani