Macitidwe 13:8 BL92

8 Koma Elima watsengayo (pakuti dzina lace litera posandulika) anawakaniza, nayesa kupatutsa kazembe asakhulupire.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 13

Onani Macitidwe 13:8 nkhani