Macitidwe 14:17 BL92

17 Koma sanadzisiyira iye mwini wopanda umboni, popeza anacita zabwino, nakupatsani inu zocokera kumwamba mvulaodi nyengoza zipatso, ndi kudzaza mitima yanu ndi cakudya ndicikondwero.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 14

Onani Macitidwe 14:17 nkhani