19 Ndipo anafika kumeneko Ayuda kucokera ku Antiokeya ndi Ikoniyo; nakopa makamu, ndipo anamponya Paulomiyala, namguzira kunja kwa mudzi; namuyesa kuti wafa.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 14
Onani Macitidwe 14:19 nkhani