Macitidwe 14:23 BL92

23 Ndipo pamene anawaikira akuru mosankha mu Mpingo Mpingo, ndi kupemphera pamodzi ndi kusala kudya, anaikiza iwo kwa Ambuye amene anamkhulupirirayo.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 14

Onani Macitidwe 14:23 nkhani