5 Ndipo pamene panakhala cigumukiro ca Ahelene ndi ca Ayuda ndi akuru ao, ca kuwacitira cipongwe ndi kuwaponya miyala,
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 14
Onani Macitidwe 14:5 nkhani