10 Nanga bwanji tsopano mulikumuyesa Mulungu, kuti muike pa khosi la akuphunzira gori, limene sanatha kunyamula kapena makolo athu kapena ife?
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 15
Onani Macitidwe 15:10 nkhani