12 Ndipo khamu lonse linatonthola; ndipo anamvera Bamaba ndi Paulo alikubwerezanso zizindikiro ndi zozizwitsa zimene Mulungu anacita nao pa amitundu.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 15
Onani Macitidwe 15:12 nkhani