19 Cifukwa cace ine ndiweruza, kuti tisabvute a mwa amitundu amene anatembenukira kwa Mulungu,
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 15
Onani Macitidwe 15:19 nkhani