21 Pakuti Mose, kuyambira pa mibadwo yakale ali nao m'midzi yonse amene amlalikira, akuwerenga mau ace m'masunagoge masabata onse.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 15
Onani Macitidwe 15:21 nkhani