3 Ndipo iwo anaperekezedwa ndi Mpingo, napita pa Foinike ndi Samariya, nafotokozera cisanduliko ca amitundu; nakondweretsa kwambiri abale onse.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 15
Onani Macitidwe 15:3 nkhani