Macitidwe 15:39 BL92

39 Ndipo panali kupsetsana mtima, kotero kuti analekana wina ndi mnzace; ndipo Bamaba anatenga Marko, nalowa n'ngalawa, nanka ku Kupro.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 15

Onani Macitidwe 15:39 nkhani