Macitidwe 15:7 BL92

7 Ndipo pamene panali mafunsano ambiri, Petro anaimirira, nati kwa iwo, Abale, mudziwa kuti poyamba Mulungu anasankha mwa inu, kuti m'kamwa mwanga amitundu amve mau a Uthenga Wabwino, nakhulupire.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 15

Onani Macitidwe 15:7 nkhani