Macitidwe 16:15 BL92

15 Pamene anabatizidwa iye ndi a pabanja pace anatidandaulira ife, kuti, Ngati mwandiyesera ine wokhulupirika kwa Ambuye, mulowe m'nyumba yanga, mugone m'menemo. Ndipo anatiumiriza ife.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 16

Onani Macitidwe 16:15 nkhani