Macitidwe 16:28 BL92

28 Koma Paulo anapfuula ndi mau akuru, nati, Usadzipweteka wekha; tonse tiri muno.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 16

Onani Macitidwe 16:28 nkhani