Macitidwe 16:3 BL92

3 Iyeyo Paulo anafuna kuti amuke naye, ndipo anamtenga, namdula, cifukwa ca Ayuda amene anakhala m'maikomo; pakuti onse anadziwa kuti atate wace anali Mhelene.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 16

Onani Macitidwe 16:3 nkhani