11 Amenewa anali mfulu koposa a m'Tesalonika, popeza analandira mau ndi kufunitsa kwa mtima wonse, nasanthula m'malembo masiku onse, ngati zinthu zinali zotero.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 17
Onani Macitidwe 17:11 nkhani