13 Koma pamene Ayuda a ku Tesalonika anazindikira kuti mau a Mulungu analalikidwa ndi Paulo ku Bereyanso, anadza komwekonso, nautsa, nabvuta makamu.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 17
Onani Macitidwe 17:13 nkhani