15 Koma iwo amene anaperekeza Paulo anadza naye kufikira ku Atene; ndipo polandira iwo lamulo la kwa Sila ndi Timoteo kuti afulumire kudza kwa iye ndi cangu conse, anacoka.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 17
Onani Macitidwe 17:15 nkhani