29 Popeza tsono tiri mbadwa za Mulungu, sitiyenera kulingalira kuti umulungu uli wofanafana ndi golidi, kapena siliva, kapena mwala, woloca ndi luso ndi zolingalira za anthu.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 17
Onani Macitidwe 17:29 nkhani