34 Koma ena anadziphatika kwa iye, nakhulupira; mwa iwonso munali Dionisiyo Mareopagi, ndi mkazi dzina lace Damarisi, ndi ena pamodzi nao.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 17
Onani Macitidwe 17:34 nkhani