Macitidwe 18:26 BL92

26 ndipo iye anayamba kulankhula molimba mtima m'sunagoge, koma pamene anamumva iye Priskila ndi Akula, anamtenga, namfotokozera njira ya Mulungu mosamalitsa.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 18

Onani Macitidwe 18:26 nkhani