3 ndipo popeza anali wa nchito imodzimodzi, anakhala nao, ndipo iwowa anagwira nchito; pakuti nchito yao inali yakusoka mahema.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 18
Onani Macitidwe 18:3 nkhani