16 Ndipo munthu, mwa iye amene munali mzimu woipa, anawalumphira nawaposa, nawalaka onse awiriwo, kotero kuti anathawa m'nyumba amarisece ndi olasidwa.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 19
Onani Macitidwe 19:16 nkhani