Macitidwe 19:21 BL92

21 Ndipo zitatha izi, Paulo anatsimikiza mu mzimu wace, atapita pa Makedoniya ndi Akaya, kunka ku Yerusalemu, kuti, Nditamuka komweko ndiyenera kuonanso ku Roma.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 19

Onani Macitidwe 19:21 nkhani