Macitidwe 19:25 BL92

25 amenewo iye anawasonkhanitsa pamodzi ndi amisiri a nchito yomweyo, nati, Amuna inu, mudziwa kuti ndi malonda awa ife tipeza cuma cathu.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 19

Onani Macitidwe 19:25 nkhani