38 Ngati tsono Demetriyo ndi amisiri okhala naye, ali ndi mlandu ndi munthu, mabwalo a mirandu alipo, ndi ziwanga ziripo; anenezane.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 19
Onani Macitidwe 19:38 nkhani