Macitidwe 19:4 BL92

4 Ndipo anati Paulo, Yohane anabatiza ndi ubatizo wa kutembenuka mtima, nati kwa anthu, kuti amkhulupirire iye amene adzadza pambuyo pace, ndiye Yesu.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 19

Onani Macitidwe 19:4 nkhani