Macitidwe 2:14 BL92

14 Koma Petro, anaimirira pamodzi ndi khumi ndi mmodziwo, nakweza mau ace, nanena kwa iwo, nati, Amuna inu Ayuda, ndi inu nonse akukhala kwanu m'Yerusalemu, ici cizindikirike kwa inu, ndi po cherani khutu mau anga.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 2

Onani Macitidwe 2:14 nkhani