Macitidwe 2:17 BL92

17 Ndipo kudzali m'masiku otsiriza, anena Mulungu,Ndidzathira ca Mzimu wansa pa thupi liri lonse,Ndipo ana anu amuna, ndi akazi adzanenera,Ndipo anyamata anu adzaona masomphenya,Ndi akulu anu adzalota maloto;

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 2

Onani Macitidwe 2:17 nkhani