Macitidwe 2:30 BL92

30 Potero, pokhala mneneri iye, ndi kudziwa kuti ndi Iumbiro anamlumbirira Mulungu, kuti mwa cipatso ca m'cuuno mwace adzakhazika wina pa mpando wacifumu wace;

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 2

Onani Macitidwe 2:30 nkhani