Macitidwe 2:4 BL92

4 Ndipo anadzazidwa onse ndi Mzimu Woyera, nayamba kulankhula ndi malilime ena, monga Mzimu anawalankhulitsa.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 2

Onani Macitidwe 2:4 nkhani