Macitidwe 20:1 BL92

1 Ndipo litaleka phokoso, Paulo anaitana ophunzirawo, ndipo m'mene anawacenjeza, analawirana nao, naturuka kunka ku Makedoniya.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 20

Onani Macitidwe 20:1 nkhani