28 Tadzicenjerani nokha, ndi gulu lonse, pamenepo Mzimu Woyera anakuikani oyang'anira, kuti muwete Eklesia wa Mulungu, umene anaugula ndi mwazi wa iye yekha.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 20
Onani Macitidwe 20:28 nkhani