Macitidwe 20:32 BL92

32 Ndipo tsopano ndikuikizani kwa Mulungu, ndi kwa mau a cisomo cace, cimene ciri ndi mphamvu yakumangirira ndi kupatsa inu colowa mwa onse oyeretsedwa.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 20

Onani Macitidwe 20:32 nkhani